Lumikizanani ndi anthu, malo, ndiponso zikhalidwe popanda vuto la chinenero

Masulirani ndi kamera yanu

Ingolozetsani kamera yanu ndipo masulirani pompopompo zomwe mukuona

Palibe intaneti? Musadandaule.

Chitani dawunilodi chinenero kuti mumasulire popanda kulumikizidwa ku intaneti

Yambani kukambirana

Lankhulani ndi munthu amene amalankhula chinenero china

Foni ya Pixel yomwe ikusonyeza njira ya njinga yomwe ili ndi mawu akuti 'imani!.' omwe amasuliridwa kuchokera mu Chijapanizi kupita ku Chingelezi mothandizidwa ndi zizindikiro zooneka mosiyanasiyana Foni ya Pixel yomwe ikusonyeza kuti Ingathe Kuchita Dawunilodi Zomasulira Popanda Intaneti mothandizidwa ndi zizindikiro zooneka mosiyanasiyana Foni ya Pixel yomwe ikusonyeza kuti ingathe Kuchita Zokambirana Pomasulira mothandizidwa ndi zizindikiro zooneka mosiyanasiyana

Masulirani m'zinenero zingapo pa nthawi yofanana mawu olankhulidwa

Yatsani Transcribe kuti mumvetse zomwe zikulankhulidwa

Masulirani kuchokera mu pulogalamu iliyonse

Mosasamala kanthu za pulogalamu yomwe mukugwiritsa ntchito, ingokoperani mawu ndi kudina kuti mumasulire

Tayipani, lankhulani, kapena lembani pamanja

Gwiritsani ntchito gawo la mawu olankhulidwa kapena olemba pamanja ndiponso mawu amene sapezeka pa kiyibodi yanu

Foni ya Pixel yomwe ikusonyeza kuti Zomasulira zingathe kuchita Kulemba Mawu Olankhulidwa mothandizidwa ndi zizindikiro zooneka mosiyanasiyana Foni ya Pixel yomwe ikusonyeza kuti ingathe Kumasulira Pongodina mothandizidwa ndi zizindikiro za maonekedwe osiyanasiyana Foni ya Pixel yomwe ikusonyeza kuti ingathe Zomasulira zingathe Kulembedwa Pamanja mothandizidwa ndi zizindikiro zooneka mosiyanasiyana

Zasungidwa

Kumasulira Dokyumenti

Kumasulira Webusaiti

Sungani zomasulira zanu

Sungani mawu kapena masentensi ndipo mutha kuwapeza mosavuta pogwiritsira ntchito chipangizo chilichonse

Chithunzi cha laputopu chomwe chikusonyeza Phrasebook ya Zomasulira mothandizidwa ndi zizindikiro zooneka mosiyanasiyana

Kodi mudokyumentiyo muli uthenga wotani?

Chitani apulodi mafailo anu kuti muthe kuwamasulira mosavuta popanda kusokoneza fomati yawo

Chithunzi cha laputopu chomwe chikusonyeza kuti Zomasulira zingathe Kumasulira Dokyumenti mothandizidwa ndi zizindikiro zooneka mosiyanasiyana

Masulirani mawebusaiti

Mukufuna kumasulira tsamba lonse la pa intaneti? Ingolembani URL kuti mumasulire tsamba lonse la pa intaneti.

Chithunzi cha laputopu chomwe chikusonyeza kuti Zomasulira zingathe Kumasulira Webusaiti mothandizidwa ndi zizindikiro zooneka mosiyanasiyana

Yesani Zomasulira za Google

Yambani kugwiritsira ntchito Zomasulira za Google mu browser. Kapena chitani sikani khodi ya QR yomwe ili m'munsiyi kuti muchite dawunilodi pulogalamu yomwe muzigwiritsa ntchito pa chipangizo chanu.

Chitani dawunilodi pulogalamu kuti muzitha kudziwa zosiyanasiyana za m'dzikoli komanso kulankhulana ndi anthu a m'zinenero zisiyanasiyana.

Pezani pulogalamuyi