Konzani Zomasulira za Google

Konzani Zomasulira

Thandizani kukonza Zomasulira za Google muzilankhulo zimene mumalankhula. Thandizani ku Gulu Lomasulira kuti muthandize anthu padziko lonse kudziwa chinenero chanu.

YAMBANIPO

Thandizirani mu Zomasulira za Google

Lembani mopanda kanthumo kapena sankhani yankho lolondola

Timakusonyezani mawu, kenako inuyo mumamasulira. Kapena mukhoza kungodina ndipo tikusonyezani mawu osiyanasiyana amene tikuganiza kuti ndi kumasulira kwake, ndipo inuyo mutiuza ngati ali olondola kapena osalondola.

Get Recognized

Yesetsani kuti mudziwike ndiponso mupeze mabaji

Muli m'gulu la 100 Club, ndi kupitirira: nthawi iliyonse imene mwathandiza, mumachulukitsa mwayi wanu wopeza baji yotsatira.

Bring languages to life

Chititsani kuti zilankhulo zikhale zamoyo

Gulu Lomasulira ndi gawo lalikulu la ndondomeko yathu yoikira zinenero zatsopano mu Zomasulira za Google. Ngati mumalankhula chinenero chimene tikumasulira, mungatithandize kuti tiike chinenerocho m'gulu la zinenero zina.